-
Yoswa 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Gulu la asilikali onyamula zida linkayenda patsogolo pa ansembe oimba malipenga, pamene gulu lina la asilikali linkabwera pambuyo pa Likasa, uku malipenga aja akuimbidwa mosalekeza.
-