Yoswa 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazisirire nʼkuzitenga+ chifukwa mukatero, mudzabweretsa tsoka pamsasa wa Isiraeli ndipo nawonso udzakhala chinthu choyenera kuwonongedwa.+
18 Koma zinthu zoyenera kuwonongedwa musamale nazo,+ kuopera kuti mungazisirire nʼkuzitenga+ chifukwa mukatero, mudzabweretsa tsoka pamsasa wa Isiraeli ndipo nawonso udzakhala chinthu choyenera kuwonongedwa.+