Yoswa 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi anthu okalamba omwe. Anaphanso ngʼombe, nkhosa ndi abulu.+
21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi anthu okalamba omwe. Anaphanso ngʼombe, nkhosa ndi abulu.+