Yoswa 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yoswa anauza amuna awiri aja amene anawatuma kukafufuza zokhudza dzikolo, kuti: “Pitani kunyumba kwa hule uja ndipo mukamutulutse limodzi ndi onse amene ali mʼnyumba mwake, mogwirizana ndi zimene munalumbira kwa iye.”+
22 Yoswa anauza amuna awiri aja amene anawatuma kukafufuza zokhudza dzikolo, kuti: “Pitani kunyumba kwa hule uja ndipo mukamutulutse limodzi ndi onse amene ali mʼnyumba mwake, mogwirizana ndi zimene munalumbira kwa iye.”+