Yoswa 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atatero, anatentha mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo. Koma siliva, golide ndiponso zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anakaziika mosungiramo chuma cha Yehova.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:24 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, tsa. 7
24 Atatero, anatentha mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo. Koma siliva, golide ndiponso zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anakaziika mosungiramo chuma cha Yehova.+