Yoswa 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yoswa anangosiya Rahabi hule uja limodzi ndi anthu amʼnyumba ya bambo ake komanso onse amene anali naye.+ Mayiyo akukhalabe ndi Aisiraeli mpaka lero+ chifukwa anabisa anthu amene Yoswa anawatuma kukafufuza zokhudza Yeriko.+
25 Yoswa anangosiya Rahabi hule uja limodzi ndi anthu amʼnyumba ya bambo ake komanso onse amene anali naye.+ Mayiyo akukhalabe ndi Aisiraeli mpaka lero+ chifukwa anabisa anthu amene Yoswa anawatuma kukafufuza zokhudza Yeriko.+