Yoswa 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa nthawiyo Yoswa analumbira* kuti: “Munthu amene adzamangenso mzinda wa Yerikowu adzakhale wotembereredwa pamaso pa Yehova. Akadzangoyala maziko ake, mwana wake woyamba adzafe, ndipo akadzaika zitseko zapageti, mwana wake wotsiriza adzafe.”+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:26 Nsanja ya Olonda,9/15/1998, ptsa. 21-22
26 Pa nthawiyo Yoswa analumbira* kuti: “Munthu amene adzamangenso mzinda wa Yerikowu adzakhale wotembereredwa pamaso pa Yehova. Akadzangoyala maziko ake, mwana wake woyamba adzafe, ndipo akadzaika zitseko zapageti, mwana wake wotsiriza adzafe.”+