-
Yoswa 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Amunawo atabwerako anauza Yoswa kuti: “Musachite kutumiza anthu onse kumeneko. Amuna pafupifupi 2,000 kapena 3,000, akhoza kugonjetsa Ai. Musatopetse anthu onse kuti apite kumeneko, chifukwa kuli anthu ochepa.”
-