Yoswa 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho amuna pafupifupi 3,000 okha anapita ku Ai, koma anathamangitsidwa ndi amuna a kumeneko.+