-
Yoswa 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo amuna a Chiisiraeli 36 anaphedwa. Anthu a ku Ai anawathamangitsa kuchokera pageti kutsetsereka mpaka kukafika ku Sebarimu. Ndipo ankawapha mʼnjira yonse. Zitatero, Aisiraeli anachita mantha kwambiri.
-