-
Yoswa 7:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zimenezi zitachitika, Yoswa anangʼamba zovala zake ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi patsogolo pa Likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, nʼkumadzithira fumbi kumutu.
-