-
Yoswa 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndipo Yoswa anati: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, nʼchifukwa chiyani mwalola kuti anthu ayende mtunda wonsewu mpaka kuwoloka mtsinje wa Yorodano, nʼkudzatipereka mʼmanja mwa Aamori kuti atiphe? Zikanakhala bwino tikanangokhala kutsidya lina lija la Yorodano!
-