Yoswa 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+
12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+