Yoswa 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene apezeke ndi zinthu zoyenera kuwonongedwazo, adzatenthedwa ndi moto,+ limodzi ndi banja lake komanso zinthu zake zonse. Adzatenthedwa chifukwa waphwanya pangano+ la Yehova ndiponso wachita choipa chochititsa manyazi mu Isiraeli.”’”
15 Amene apezeke ndi zinthu zoyenera kuwonongedwazo, adzatenthedwa ndi moto,+ limodzi ndi banja lake komanso zinthu zake zonse. Adzatenthedwa chifukwa waphwanya pangano+ la Yehova ndiponso wachita choipa chochititsa manyazi mu Isiraeli.”’”