Yoswa 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anauza mabanja a mʼfuko la Yuda kufika pamaso pa Mulungu, ndipo banja la Zera+ linasankhidwa. Kenako anauza banja la Zera kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense payekhapayekha, ndipo Zabidi anasankhidwa.
17 Kenako anauza mabanja a mʼfuko la Yuda kufika pamaso pa Mulungu, ndipo banja la Zera+ linasankhidwa. Kenako anauza banja la Zera kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense payekhapayekha, ndipo Zabidi anasankhidwa.