-
Yoswa 7:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli, ulula kwa iye. Tandiuza chonde, wachita chiyani? Usandibisire.”
-