-
Yoswa 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Akani anayankha Yoswa kuti: “Ndithudi, ineyo ndi amene ndachimwira Yehova Mulungu wa Isiraeli. Zimene ndinachita ndi izi:
-