-
Yoswa 7:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pakati pa zinthu zoyenera kuwonongedwa ndinaonapo chovala chokongola komanso chamtengo wapatali cha ku Sinara,+ masekeli* a siliva 200 komanso mtanda umodzi wa golide wolemera masekeli 50. Nditaziona ndinazisirira ndipo ndinazitenga. Panopa chovalacho ndi ndalamazo ndazikumbira pansi, pakati pa tenti yanga, ndipo ndalamazo zili pansi pa chovalacho.”
-