-
Yoswa 7:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Nthawi yomweyo Yoswa anatuma anthu, amene anathamangira kutentiko. Iwo anachipezadi chovalacho mʼhema wake, ndipo ndalama zinali pansi pake.
-