Yoswa 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anati: “Nʼchifukwa chiyani watibweretsera tsoka?*+ Lero Yehova akubweretsera iweyo tsoka.” Atatero, Aisiraeli onse anayamba kuwaponya miyala+ anthuwo ndipo kenako anawatentha ndi moto.+ Umu ndi mmene anawaphera, anawaponya miyala.
25 Ndiyeno Yoswa anati: “Nʼchifukwa chiyani watibweretsera tsoka?*+ Lero Yehova akubweretsera iweyo tsoka.” Atatero, Aisiraeli onse anayamba kuwaponya miyala+ anthuwo ndipo kenako anawatentha ndi moto.+ Umu ndi mmene anawaphera, anawaponya miyala.