Yoswa 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero. Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Nʼchifukwa chake malowo amatchedwa chigwa cha Akori* mpaka lero.
26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero. Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Nʼchifukwa chake malowo amatchedwa chigwa cha Akori* mpaka lero.