Yoswa 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo ndipo upite kukamenyana ndi mzinda wa Ai. Dziwa kuti mfumu ya Ai ndaipereka kwa iwe limodzi ndi anthu ake, mzinda wake komanso dera lake lonse.+
8 Kenako Yehova anauza Yoswa kuti: “Usaope kapena kuchita mantha.+ Tenga amuna onse ankhondo ndipo upite kukamenyana ndi mzinda wa Ai. Dziwa kuti mfumu ya Ai ndaipereka kwa iwe limodzi ndi anthu ake, mzinda wake komanso dera lake lonse.+