-
Yoswa 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Tsopano mfumu ya Ai itaona zimenezo, nthawi yomweyo mfumuyo ndi amuna amumzindawo anakonzeka kuti akamenyane ndi Aisiraeli. Anadzuka mʼmamawa kukakumana nawo pamalo ena pomwe ankatha kuona bwino chigwa cha mʼchipululu. Koma mfumuyo sinadziwe kuti asilikali ena anali atabisala kumbuyo kwa mzindawo.
-