-
Yoswa 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Zitatero, anthu onse amumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzindawo.
-