-
Yoswa 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Panalibe mwamuna ndi mmodzi yemwe amene anatsala ku Ai ndi ku Beteli. Onse anapita kukathamangitsa Aisiraeli, ndipo mageti a mzindawo anangowasiya osatseka.
-