Yoswa 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina* la Yorodano, omwe ndi Mfumu Sihoni+ ya ku Hesiboni ndi Mfumu Ogi+ ya ku Basana, imene inali ku Asitaroti.
10 Tamvanso zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kutsidya lina* la Yorodano, omwe ndi Mfumu Sihoni+ ya ku Hesiboni ndi Mfumu Ogi+ ya ku Basana, imene inali ku Asitaroti.