Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Aisiraeliwo ananyamuka nʼkukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibiyoni,+ Kefira, Beeroti ndi Kiriyati-yearimu.+
17 Aisiraeliwo ananyamuka nʼkukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibiyoni,+ Kefira, Beeroti ndi Kiriyati-yearimu.+