Yoswa 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano mukhala anthu otembereredwa.+ Mukhala akapolo ndipo muzitola nkhuni ndi kutungira madzi nyumba ya Mulungu wanga.” Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:23 Galamukani!,5/2012, tsa. 18
23 Tsopano mukhala anthu otembereredwa.+ Mukhala akapolo ndipo muzitola nkhuni ndi kutungira madzi nyumba ya Mulungu wanga.”