Yoswa 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:27 Nsanja ya Olonda,12/15/1986, ptsa. 24-25
27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+