-
Yoswa 10:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Adoni-zedeki mfumu ya Yerusalemu anamva zoti Yoswa walanda mzinda wa Ai nʼkuuwononga. Anamva kuti wawononga mzindawo ndi kupha mfumu yake+ ngati mmene anachitira ndi mzinda wa Yeriko ndi mfumu yake.+ Anamvanso kuti anthu a ku Gibiyoni agwirizana za mtendere ndi Aisiraeli+ ndipo akukhala pakati pawo. Atangomva zimenezi,
-