Yoswa 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zitatero, amuna a ku Gibiyoni anatumiza uthenga kwa Yoswa kumsasa ku Giligala,+ kuti: “Bwerani msanga mudzatithandize ndi kutipulumutsa. Mafumu onse a Aamori okhala kudera lamapiri asonkhana kuti amenyane nafe. Musatisiye tokha ife akapolo anu.”+
6 Zitatero, amuna a ku Gibiyoni anatumiza uthenga kwa Yoswa kumsasa ku Giligala,+ kuti: “Bwerani msanga mudzatithandize ndi kutipulumutsa. Mafumu onse a Aamori okhala kudera lamapiri asonkhana kuti amenyane nafe. Musatisiye tokha ife akapolo anu.”+