Yoswa 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova anasokoneza adaniwo pamaso pa Aisiraeli.+ Ndipo Aisiraeli anapha adani ambirimbiri ku Gibiyoni. Anawathamangitsa kulowera kuchitunda cha Beti-horoni ndipo anapitiriza kuwapha mpaka kukafika ku Azeka ndi ku Makeda.
10 Yehova anasokoneza adaniwo pamaso pa Aisiraeli.+ Ndipo Aisiraeli anapha adani ambirimbiri ku Gibiyoni. Anawathamangitsa kulowera kuchitunda cha Beti-horoni ndipo anapitiriza kuwapha mpaka kukafika ku Azeka ndi ku Makeda.