Yoswa 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi sunayende mpaka mtunduwo utalanga adani ake. Kodi sizinalembedwe mʼbuku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, ndipo linaimabe choncho pafupifupi maola 24.* Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 3212/1/2004, tsa. 1112/15/1986, tsa. 26
13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi sunayende mpaka mtunduwo utalanga adani ake. Kodi sizinalembedwe mʼbuku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, ndipo linaimabe choncho pafupifupi maola 24.*