-
Yoswa 10:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Aisiraeli onse anabwerera bwinobwino kwa Yoswa kumsasa, ku Makeda. Ndipo palibe munthu amene ananena zamtopola kwa Aisiraeliwo.
-