Yoswa 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo anatseguladi phangalo nʼkutulutsa mafumu 5 aja: Mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi ndi mfumu ya ku Egiloni.+
23 Iwo anatseguladi phangalo nʼkutulutsa mafumu 5 aja: Mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi ndi mfumu ya ku Egiloni.+