Yoswa 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa zimenezi ndi zimene Yehova azichitira adani anu onse amene muzimenyana nawo.”+
25 Ndiyeno Yoswa anawauza kuti: “Musaope kapena kuchita mantha.+ Khalani olimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu, chifukwa zimenezi ndi zimene Yehova azichitira adani anu onse amene muzimenyana nawo.”+