Yoswa 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti awatsitse pamitengoyo+ nʼkuwaponyera mʼphanga limene anabisalamo lija. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, ndipo ilipobe mpaka lero.
27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti awatsitse pamitengoyo+ nʼkuwaponyera mʼphanga limene anabisalamo lija. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, ndipo ilipobe mpaka lero.