Yoswa 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse anachoka ku Libina nʼkupita ku Lakisi.+ Atafika anamanga msasa nʼkuyamba kumenyana ndi anthu akumeneko.
31 Kenako Yoswa ndi Aisiraeli onse anachoka ku Libina nʼkupita ku Lakisi.+ Atafika anamanga msasa nʼkuyamba kumenyana ndi anthu akumeneko.