Yoswa 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yehova anapereka Lakisi mʼmanja mwa Isiraeli, moti analanda mzindawo pa tsiku lachiwiri. Anapha ndi lupanga anthu onse amumzindawo,+ ngati mmene anachitira ku Libina.
32 Yehova anapereka Lakisi mʼmanja mwa Isiraeli, moti analanda mzindawo pa tsiku lachiwiri. Anapha ndi lupanga anthu onse amumzindawo,+ ngati mmene anachitira ku Libina.