Yoswa 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zitatero Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza anthu a ku Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.
33 Zitatero Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza anthu a ku Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.