Yoswa 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anaitanitsanso Akanani+ omwe ankakhala kumʼmawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti, Aperezi ndi Ayebusi akudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe ankakhala mʼmunsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.
3 Anaitanitsanso Akanani+ omwe ankakhala kumʼmawa ndi kumadzulo, ndiponso Aamori,+ Ahiti, Aperezi ndi Ayebusi akudera lamapiri. Komanso anaitanitsa Ahivi+ omwe ankakhala mʼmunsi mwa phiri la Herimoni+ ku Mizipa.