Yoswa 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho mafumuwo pamodzi ndi magulu awo onse ankhondo anabwera. Anali ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja. Ndipo anali ndi mahatchi* komanso magaleta* ankhondo ambirimbiri.
4 Choncho mafumuwo pamodzi ndi magulu awo onse ankhondo anabwera. Anali ambiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja. Ndipo anali ndi mahatchi* komanso magaleta* ankhondo ambirimbiri.