Yoswa 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ chifukwa mawa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundule*+ ndipo magaleta awo udzawatenthe.”
6 Ndiyeno Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ chifukwa mawa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundule*+ ndipo magaleta awo udzawatenthe.”