Yoswa 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso Yoswa anabwerera nʼkukalanda mzinda wa Hazori ndipo anapha mfumu yake ndi lupanga,+ chifukwa poyamba mzinda wa Hazori unali likulu la maufumu onsewa.
10 Komanso Yoswa anabwerera nʼkukalanda mzinda wa Hazori ndipo anapha mfumu yake ndi lupanga,+ chifukwa poyamba mzinda wa Hazori unali likulu la maufumu onsewa.