Yoswa 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, nʼkupha mafumu ake onse ndi lupanga+ mogwirizana ndi zimene Mose, mtumiki wa Yehova, analamula.
12 Yoswa analanda mizinda yonse ya mafumuwa, nʼkupha mafumu ake onse ndi lupanga+ mogwirizana ndi zimene Mose, mtumiki wa Yehova, analamula.