-
Yoswa 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Komabe mizinda yonse imene inamangidwa pamalo okwera, Aisiraeli sanaitenthe. Mzinda wa Hazori wokha ndi umene Yoswa anautentha.
-