Yoswa 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Analandanso dera lochokera kuphiri la Halaki lomwe lili moyangʼanizana ndi Seiri mpaka kukafika ku Baala-gadi,+ kuchigwa cha Lebanoni mʼmunsi mwa phiri la Herimoni.+ Yoswa anagonjetsa mafumu awo onse nʼkuwapha.
17 Analandanso dera lochokera kuphiri la Halaki lomwe lili moyangʼanizana ndi Seiri mpaka kukafika ku Baala-gadi,+ kuchigwa cha Lebanoni mʼmunsi mwa phiri la Herimoni.+ Yoswa anagonjetsa mafumu awo onse nʼkuwapha.