Yoswa 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova ndi amene analola kuti anthuwa aumitse mitima yawo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndipo asawamvere chisoni,+ koma awatheretu mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+
20 Yehova ndi amene analola kuti anthuwa aumitse mitima yawo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Anatero kuti iye awawononge ndipo asawamvere chisoni,+ koma awatheretu mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+