Yoswa 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawiyo Yoswa anapita nʼkukapha Aanaki+ onse kudera lamapiri, ku Heburoni, ku Debiri, ku Anabi, kudera lonse lamapiri la Yuda ndiponso kudera lonse lamapiri la Isiraeli. Yoswa anapha Aanaki onsewo nʼkuwononga mizinda yawo.+
21 Pa nthawiyo Yoswa anapita nʼkukapha Aanaki+ onse kudera lamapiri, ku Heburoni, ku Debiri, ku Anabi, kudera lonse lamapiri la Yuda ndiponso kudera lonse lamapiri la Isiraeli. Yoswa anapha Aanaki onsewo nʼkuwononga mizinda yawo.+