Yoswa 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Yoswa analanda dziko lonse mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza Mose.+ Kenako Yoswa anagawa dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo, mogwirizana ndi mafuko awo.+ Ndipo mʼdziko lonselo munalibenso nkhondo.+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, tsa. 11
23 Choncho Yoswa analanda dziko lonse mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza Mose.+ Kenako Yoswa anagawa dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo, mogwirizana ndi mafuko awo.+ Ndipo mʼdziko lonselo munalibenso nkhondo.+